Proverbs 15:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wabwino amaganizira za m'mene ayankhire, koma pakamwa pa munthu woipa pamatuluka mau oipa okhaokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wa wolungama uganizira za mayankhidwe; koma m'kamwa mwa ochimwa mutsanulira zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wolungama amaganizira za mmene ayankhire, koma pakamwa pa munthu woyipa pamatulutsa mawu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wa wolungama uganizira za mayankhidwe; Koma m'kamwa mwa ocimwa mutsanulira zoipa.