Proverbs 15:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amakhala kutali ndi anthu oipa mtima, koma amamva pemphero la anthu achilungamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova atalikira oipa; koma pemphero la olungama alimvera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amakhala kutali ndi anthu oyipa, koma amamva pemphero la anthu olungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova atarikira oipa; Koma pemphero la olungama alimvera.