Proverbs 15:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso okondwa amasangalatsa mtima, ndipo uthenga wabwino umalimbitsa munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuunika kwa maso kukondweretsa mtima; ndipo pomveka zabwino mafupa amatenga uwisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwala kwa maso kumasangalatsa mtima ndipo uthenga wabwino umalimbitsa munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuunika kwa maso kukondweretsa mtima; Ndipo pomveka zabwino mafupa amatenga uwisi.