Proverbs 15:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wochita chilungamo amakhala ndi chuma chambiri, koma zimene woipa amapindula zimamgwetsa m'mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'nyumba ya wolungama muli katundu wambiri; koma m'phindu la woipa muli vuto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wolungama amakhala ndi chuma chambiri, zimene woyipa amapindula nazo zimamugwetsa mʼmavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'nyumba ya wolungama muli katundu wambiri; Koma m'phindu la woipa muli bvuto,