Proverbs 15:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakamwa pa anthu anzeru pamafalitsa nzeru, koma mitima ya zitsiru siitero.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Milomo ya anzeru iwanditsa nzeru, koma mtima wa opusa suli wolungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakamwa pa anthu anzeru pamafalitsa nzeru; koma mitima ya zitsiru sitero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Milomo ya anzeru iwanditsa nzeru, Koma mtima wa opusa suli wolungama.