Proverbs 15:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nsembe ya anthu oipa mtima imamuipira Chauta, koma pemphero la anthu olungama limamkondweretsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsembe ya oipa inyansa Yehova; koma pemphero la oongoka mtima limkondweretsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nsembe za anthu oyipa zimamunyansa Yehova, koma amakondwera ndi pemphero la anthu owona mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsembe ya oipa inyansa Yehova; Koma pemphero la oongoka mtima limkondweretsa.