Proverbs 15:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zochita za anthu oipa zimamnyansa Chauta, koma wochita zachilungamo Chauta amamkonda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njira ya oipa inyansa Yehova; koma akonda wolondola chilungamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ntchito za anthu oyipa zimamunyansa Yehova koma amakonda amene amafunafuna chilungamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njira ya oipa inyansa Yehova; Koma akonda wolondola cilungamo.