Proverbs 2:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, uvomere mau anga, ndi kusunga bwino malamulo anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, ukalandira mau anga, ndi kusunga malamulo anga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, ngati ulandira mawu anga ndi kusunga malamulo anga mu mtima mwako,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, ukalandira mau anga, Ndi kusunga malamulo anga;