Proverbs 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuganiziratu zam'tsogolo kudzakusunga, kumvetsa zinthu kudzakuteteza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kulingalira kudzakudikira, kuzindikira kudzakutchinjiriza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuganizira bwino za mʼtsogolo kudzakusunga; kumvetsa zinthu bwino kudzakuteteza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kulingalira kudzakudikira, Kuzindikira kudzakucinjiriza;