Proverbs 2:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti nyumba yake imatsenderekera ku imfa, njira zake zimamufikitsa kwa anthu akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyumba yake itsikira kuimfa, ndi mayendedwe ake kwa akufa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti nyumba yake imatsetserekera ku imfa; njira zake zimamufikitsa ku manda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyumba yace itsikira kuimfa, Ndi mayendedwe ace kwa akufa;