Proverbs 2:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu oipa Mulungu adzaŵachotsa pa dziko, anthu onyenga adzaŵatulutsa m'dzikomo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma oipa adzalikhidwa m'dziko, achiwembu adzazulidwamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu oyipa adzachotsedwa mʼdzikomo, ndipo anthu onyenga adzachotsedwamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma oipa adzalikhidwa m'dziko, Aciwembu adzazulidwamo.