Proverbs 2:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikutitu upemphe mtima wozindikira zinthu, ndi kupemba kuti ukhale womvetsa zinthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ukaitananso luntha, ndi kufuulira kuti ukazindikire;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati upempha kuti uzindikire zinthu inde kupempha ndi mtima wonse kuti ukhale womvetsa zinthu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukaitananso luntha, Ndi kupfuulira kuti ukazindikire;