Proverbs 2:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja Chauta ndiye amapatsa nzeru, Iye ndiye kasupe wa kudziŵa zinthu ndi wa kumvetsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova apatsa nzeru; kudziwa ndi kuzindikira kutuluka m'kamwa mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Yehova ndiye amapereka nzeru, ndipo mʼkamwa mwake mumachokera chidziwitso ndi kumvetsa zinthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova apatsa nzeru; Kudziwa ndi kuzindikira kuturuka m'kamwa mwace;