Proverbs 2:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasungira anthu olungama nzeru zenizeni, ali ngati chishango choteteza oyenda mwaungwiro.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye asungira oongoka mtima nzeru yeniyeni; ndiye chikopa cha oyenda molunjika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olungama zinthu zimawayendera bwino chifukwa Yehova amakhala nawo. Paja Yehova ndiye chishango cha amene amayenda mwangwiro,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye asungira oongoka mtima nzeru yeniyeni; Ndiye cikopa ca oyenda molunjika;