Proverbs 20:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale mwana yemwe amadziŵika ndi ntchito zake, kuti zimene amachitazo ndi zabwino ndi zolungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngakhale mwana adziwika ndi ntchito zake; ngati ntchito yake ili yoyera ngakhale yolungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale mwana amadziwika ndi zochita zake, ngati zochita zake zili zoyera ndi zoyenera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngakhale mwana adziwika ndi nchito zace; Ngati nchito yace iri yoyera ngakhale yolungama.