Proverbs 20:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pali golide ndi miyala yambirimbiri yamtengowapatali, koma mau olankhula zanzeru ali ndi mtengo woposa zonsezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alipo golide ndi ngale zambiri; koma milomo yodziwa ndiyo chokometsera cha mtengo wapatali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pali golide ndi miyala yamtengowapatali, koma milomo yoyankhula zanzeru ndi yamtengowapatali koposa zonsezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alipo golidi ndi ngale zambiri; Koma milomo yodziwa ndiyo cokometsera ca mtengo wapatari.