Proverbs 20:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chakudya chochipeza monyenga chimamkomera munthu, koma pambuyo pake chimakasanduka ngati lubwe m'kamwa mwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zakudya za chinyengo zikondweretsa munthu; koma pambuyo pake m'kamwa mwake mudzadzala tinsangalabwi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chakudya chochipeza mwachinyengo chimukomera munthu, koma pa mapeto pake chimasanduka ngati mchenga mʼkamwa mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zakudya za cinyengo zikondweretsa munthu; Koma pambuyo pace m'kamwa mwace mudzadzala tinsangalabwi.