Proverbs 20:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukakonzekera kuchita zinthu, uziyamba wafunsa. Usanamenye nkhondo, uyambe wapempha malangizo oyenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uphungu utsimikiza zolingalira, ponya nkhondo utapanga upo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zokonzekera zimapindula utafunsira uphungu; ndipo usanamenye nkhondo yamba wapempha malangizo oyenera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uphungu utsimikiza zolingalira, Ponya nkhondo utapanga upo.