Proverbs 20:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo woopsa wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango. Amene amauputa dala mkwiyowo, amataya moyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuopsa kwa mfumu ndiko kubangula kwa mkango; womputa achimwira moyo wakewake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukali wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango; amene amawuputa mkwiyowo amataya moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuopsya kwa mfumu ndiko kubangula kwa mkango; Womputa acimwira moyo wace wace.