Proverbs 20:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi msampha kwa munthu kupereka chinthu kwa Chauta mosaganiza bwino, chifukwa mwina atha kusintha maganizo atalumbira kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kunena mwansontho, Ichi nchopatulika, kuli msampha kwa munthu, ndi kusinkhasinkha pambuyo pake atawinda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi msampha kwa munthu kuyankhula mofulumira kuti “Chinthu ichi nʼchopatulika kwa Yehova,” popeza mwina atha kusintha maganizo utalumbira kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kunena mwansontho, ici ncopatulika, kuli msampha kwa munthu, Ndi kusinkhasinkha pambuyo pace atawinda.