Proverbs 20:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchaulemu kwa munthu kumalewa mikangano, koma aliyense wopusa amakonda kulongolola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuli ulemu kwa mwamuna kupewa ndeu; koma zitsiru zonse zimangokangana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchaulemu kwa munthu kupewa mikangano, koma chitsiru chilichonse chimafulumira kulongolola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuli ulemu kwa mwamuna kupewa ndeu; Koma zitsiru zonse zimangokangana,