Proverbs 20:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mikwingwirima ndiye mankhwala ochotsa zoipa. Mikwapulo imachiza zam'katikati mwa munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mikwingwirima yopweteka ichotsa zoipa; ndi mikwapulo ilowa m'kati mwa mimba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mikwingwirima yopweteka ndiyo imachotsa zoyipa, ndipo mikwapulo ndiyo imachotsa zamʼkatikati mwa munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mikwingwirima yopweteka icotsa zoipa; Ndi mikwapulo ilowa m'kati mwa mimba.