Proverbs 20:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Waulesi sasoseratu pa nthaŵi yoyenera. Pa nthaŵi yokolola adzafunafuna dzinthu, koma sadzapeza kanthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Waulesi salima chifukwa cha chisanu; adzapemphapempha m'masika osalandira kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu waulesi satipula mʼmunda pa nthawi yoyenera; kotero pa nthawi yokolola adzafunafuna zinthu koma sadzapeza kanthu kalikonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolesi salima cifukwa ca cisanu; Adzapemphapempha m'masika osalandira kanthu.