Proverbs 20:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zolinga za mtima wa munthu zili ngati madzi ozama, ndi munthu wanzeru yekha angazitulutse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uphungu wa m'mtima mwa munthu ndiwo madzi akuya; koma munthu wozindikira adzatungapo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zolinga za mtima wa munthu zili ngati madzi akuya, munthu womvetsa zinthu ndiye yekha angawatunge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uphungu wa m'mtima mwa munthu ndiwo madzi akuya; Koma munthu wozindikira adzatungapo,