Proverbs 20:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ambiri amalankhula za kukhulupirika kwao, koma ndani angathe kumpeza munthu wokhulupirika kwenikweni?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu ambiri abukitsa yense kukoma mtima kwake; koma ndani angapeze munthu wokhulupirika?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ambiri amayankhula za kukhulupirika kwawo, koma munthu wokhulupirika angamupeze ndani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu ambiri abukitsa yense kukoma mtima kwace; Koma ndani angapeze munthu wokhulupirika?