Proverbs 20:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mfumu ikhala pa mpando wake wa chiweruzo, imazindikira ndi maso chabe anthu onse amene ali oipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu yokhala pa mpando woweruzira ipirikitsa zoipa zonse ndi maso ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu ikhala pa mpando wake wa chiweruzo, imapeta ndi maso ake anthu onse oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu yokhala pa mpando waweruzira Ipitikitsa zoipa zonse ndi maso ace.