Proverbs 22:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbiri yabwino ndi yofunika kupambana chuma chambiri, kupeza kuyanja nkopambana siliva ndi golide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbiri yabwino ifunika kopambana chuma chambiri; kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbiri yabwino ndi yofunika kuposa chuma chambiri; kupeza kuyanja nʼkwabwino kuposa siliva kapena golide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbiri yabwino ifunika kopambana cuma cambiri; Kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golidi.