Proverbs 22:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amayang'anira bwino anthu odziŵa zinthu, koma mau a anthu osakhulupirika, Iye amaŵalepheretsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maso a Yehova atchinjiriza wodziwa; koma agwetsa mau a munthu wa ziwembu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso a Yehova amakhala pa anthu odziwa bwino zinthu, koma Iye adzalepheretsa mawu a anthu osakhulupirika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maso a Yehova acinjiriza wodziwa; Koma agwetsa mau a munthu wa ziwembu.