Proverbs 22:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amapondereza osauka kuti aonjezere pa chuma chake, kapena amene amangopatsa zinthu olemera okha, adzasanduka wosauka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wotsendereza waumphawi kuti achulukitse chuma chake, ndi wopatsa wolemera kanthu, angosauka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amapondereza anthu osauka kuti awonjezere chuma chake, ndiponso amene amapereka mphatso kwa anthu olemera onsewa adzasauka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wotsendereza waumphawi kuti acurukitse cuma cace, Ndi wopatsa wolemera kanthu, angosauka.