Proverbs 22:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chidzakhala chokondwetsa ukazisunga, ndi kukhala wokonzeka kumazilankhula pa nthaŵi yake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mauwo akondweretsa ngati uwasunga m'kati mwako, ngati akhazikika pamodzi pa milomo yako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zidzakhala zokondweretsa ngati uzisunga mu mtima mwako ndi wokonzeka kuziyankhula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mauwo akondweretsa ngati uwasunga m'kati mwako, Ngati akhazikika pamodzi pa milomo yako.