Proverbs 22:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
malangizo okudziŵitsa zolungama ndi zoona, kuti ukaŵayankhe zoona amene adakutuma?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ukadziwitse ntheradi yake ya mau oona, nukabwere ndi mau oona kwa iwo amene anakutumiza?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
malangizo okudziwitsa zolungama ndi zoona ndi kuti ukawayankhe zoona amene akutumawo?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ukadziwitse ntheradi yace ya mau oona, Nukabwere ndi mau oona kwa iwo amene anakutumiza?