Proverbs 23:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukakhala pansi kuti udye ndi mfumu, uyang'ane bwino zimene zili pamaso pako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene ukhala ulinkudya ndi mkulu, zikumbukira ameneyo ali pamaso pako;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ukhala pansi kuti udye pamodzi ndi wolamulira, uyangʼane bwino zimene zili pamaso pako,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene ukhala ulinkudya ndi mkuru, Zikumbukira ameneyo ali pamaso pako;