Proverbs 23:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wako ukhale pa malangizo, ndipo makutu ako azimvetsera mau anzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lozetsa mtima wako kumwambo, ndi makutu ako ku mau anzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wako uzikhala pa malangizo ndipo makutu ako azimvetsera mawu a chidziwitso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lozetsa mtima wako kumwambo, Ndi makutu ako ku mau a nzeru.