Proverbs 23:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usamaleka kumpatsa mwambo mwana, ukamkwapula ndi tsatsa sadzafa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamane mwana chilango; pakuti ukammenya ndi nthyole safa ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usaleke kumulangiza mwana; ngati umulanga ndi chikwapu sadzafa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamane mwana cilango; Pakuti ukammenya ndi ntyole safa ai.