Proverbs 23:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, mtima wako ukakhala wanzeru, nanenso mtima wanga udzasangalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, mtima wako ukakhala wanzeru, mtima wanga wa inedi udzakondwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, ngati mtima wako ukhala wanzeru, inenso mtima wanga udzakondwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, mtima wako ukakhala wanzeru, Mtima wanga wa inedi udzakondwa;