Proverbs 23:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wako usamachita nsanje ndi anthu ochimwa, koma upitirire kumaopa Chauta tsiku ndi tsiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wako usachitire nsanje akuchimwawo; koma opabe Yehova tsiku lonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wako usachite nsanje ndi anthu ochimwa, koma uziopa Yehova tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wako usacitire nsanje akucimwawo; Koma opabe Yehova tsiku lonse;