Proverbs 23:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bambo wa mwana waulemu adzakondwa kwambiri. Wobala mwana wanzeru adzasangalala naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atate wa wolungama adzasekeradi; wobala mwana wanzeru adzakondwera naye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abambo a munthu wolungama ali ndi chimwemwe chachikulu; Wobala mwana wanzeru adzakondwera naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atate wa wolungama adzasekeradi; Wobala mwana wanzeru adzakondwera naye.