Proverbs 23:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, mtima wako ukhulupirire ine, maso ako apenyetsetse njira zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, undipatse mtima wako, maso ako akondwere ndi njira zanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, undikhulupirire ndipo maso ako apenyetsetse njira zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, undipatse mtima wako, Maso ako akondwere ndi njira zanga,