Proverbs 23:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amabisalira ngati mbala yachifwamba, ndipo chifukwa cha iyeyo amuna ambiri amasanduka osakhulupirika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti abisalira ngati wachifwamba, nachulukitsa anthu a chiwembu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amabisala ngati mbala yachifwamba, ndipo amuna amakhala osakhulupirika chifukwa cha iyeyu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti abisalira ngati wacifwamba, Nacurukitsa anthu a ciwembu.