Proverbs 23:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani ali ndi tsoka? Ndani ali ndi chisoni? Ndani ali pa mkangano? Ndani akudandaula? Ndani ali ndi zilonda zosadziŵika magwero ake? Ndani ali wofiira maso?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndani ali ndi chisoni? Ndani asauka? Ndani ali ndi makangano? Ndani ang'ung'udza? Ndani alasidwa chabe? Ndani afiira maso?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndani ali ndi tsoka? Ndani ali ndi chisoni? Ndani ali pa mkangano? Ndani ali ndi madandawulo? Ndani ali ndi zipsera zosadziwika uko zachokera? Ndani ali ndi maso ofiira?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndani ali ndi cisoni? ndani asauka? ndani ali ndi makangano? Ndani ang'ung'udza? ndani alasidwa cabe? ndani afiira maso?