Proverbs 23:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Udzakhala ngati munthu amene ali gone pakati pa nyanja, kapena ngati munthu wogona pa nsonga ya mlongoti wa ngalaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Udzafanana ndi wina wogona pakati pa nyanja, pena wogona pa nsonga ya mlongoti wa ngalawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Udzakhala ngati munthu amene ali gone pakati pa nyanja, kapena ngati munthu wogona pa msonga ya mlongoti ya ngalawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Udzafanana ndi wina wogona pakati pa nyanja, Pena wogona pa nsonga ya mlongoti wa ngalawa.