Proverbs 23:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukangopeza chuma, uwona chapita kale, pakuti chimachita ngati chamera mapiko mwadzidzidzi, nkuyamba kuuluka kunka kumwamba ngati chiwombankhanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi upenyeranji chimene kulibe? Pakuti chuma chimera mapiko, ngati mphungu youluka mumlengalenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukangoti wachipeza chumacho uwona posachedwa kuti palibepo. Chumacho chimachita ngati chamera mapiko mwadzidzidzi ndi kuwuluka kunka kumwamba ngati chiwombankhanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi upenyeranji cimene kulibe? Pakuti cuma cunera mapiko, Ngati mphungu youluka mumlengalenga.