Proverbs 24:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukanena kuti, “Ife sitidazidziŵe zimenezi,” kodi iye amene amayesa mtima, zimenezi saziwona? Kodi amene amayang'anira moyo wako sazidziŵa? Kodi sadzambwezera munthu potsata ntchito zake?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukanena, Taonani, sitinadziwa chimenechi; kodi woyesa mitima sachizindikira ichi? Ndi wosunga moyo wako kodi sachidziwa? Ndipo kodi sabwezera munthu yense monga mwa machitidwe ake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukanena kuti, “Koma ife sitinadziwe kanthu za izi,” kodi Iye amene amasanthula mtima sazindikira zimenezi? Kodi Iye amene amateteza moyo wako sazidziwa zimenezi? Kodi Iye sadzalipira munthu malingana ndi ntchito zake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukanena, Taonani, sitinadziwa cimeneci; Kodi woyesa mitima sacizindikira ici? Ndi wosunga moyo wako kodi sacidziwa? Ndipo kodi sabwezera munthu yense monga mwa macitidwe ace?