Proverbs 24:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, uzidya uchi poti ndi wabwino, madzi a m'chisa cha njuchi ndi ozuna ukaŵalaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, idya uchi pakuti ngwabwino, ndi chisa chake chitsekemera m'kamwa mwako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, uzidya uchi popeza ndi wabwino; uchi wochokera mʼchisa cha njuchi ndi wokoma ukawulawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, idya uci pakuti ngwabwino, Ndi cisa cace citsekemera m'kamwamwako;