Proverbs 24:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wabwino amagwa kasanunkaŵiri, koma amadzukirira ndithu, m'menemo anthu oipa tsoka limaŵagwera chonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti wolungama amagwa kasanu ndi kawiri, nanyamukanso; koma oipa akhumudwa pomfikira tsoka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
paja munthu wolungama akagwa kasanu nʼkawiri amadzukiriranso. Koma woyipa adzathedwa tsoka likadzawafikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti wolungama amagwa kasanu ndi kawiri, nanyamukanso; Koma oipa akhumudwa pomfikira tsoka.