Proverbs 24:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukatero Chauta adzaziwona zimenezo nadzaipidwa nazo, kenaka adzaleka kumkwiyira mdani wakoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti Yehova angaone kukondwa kwako, ndi kukuyesa koipa, ndi kuleka kumkwiyira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuopa kuti Yehova ataziona zimenezi nayipidwa nazo, angaleke kukwiyira mdaniyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti Yehova angaone kukondwa kwako, ndi kukuyesa koipa, Ndi kuleka kumkwiyira.