Proverbs 24:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa mitima yao imalingalira zandeu, ndipo pakamwa pao pamalankhula zoutsa mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti mtima wao ulingalira za chionongeko; milomo yao ilankhula za mphulupulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti mitima yawo imalingalira chiwawa, ndipo pakamwa pawo pamayankhula zoyambitsa mavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mtima wao ulingalira za cionongeko; Milomo yao ilankhula za mphulupulu.