Proverbs 24:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pajatu munthu woipa zinthu sizidzamuyendera bwino m'tsogolo, moyo wa anthu oipa adzauzima ngati nyale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti woipayo sadzalandira mphotho; nyali ya amphulupulu idzazima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
paja munthu woyipa alibe tsogolo. Moyo wa anthu oyipa adzawuzimitsa ngati nyale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti woipayo sadzalandira mphotho; Nyali ya amphulupulu idzazima.