Proverbs 24:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, uziwopa Chauta ndiponso mfumu, usagwirizane ndi anthu okonda kuŵachitira mwano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, opa Yehova ndi mfumu yomwe, osadudukira anthu osinthasintha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, uziopa Yehova ndi mfumu, ndipo usamagwirizana ndi anthu owachitira mwano,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, opa Yehova ndi mfumu yomwe, Osadudukira anthu osinthasintha.