Proverbs 24:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usakhale mboni yotsutsa mnzako popanda chifukwa, pakamwa pako pasamanena zonama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usachitire mnzako umboni womtsutsa opanda chifukwa; kodi udzanyenga ndi milomo yako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usakhale mboni yotsutsa mnzako popanda chifukwa, kapena kugwiritsa ntchito pakamwa pako kunena zachinyengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usacitire mnzako umboni womtsutsa opanda cifukwa; Kodi udzanyenga ndi milomo yako?